1 Samueli 14:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 M’masiku onse a Sauli, Afilisiti anali kupanikizidwa ndi nkhondo.+ Ndipo Sauli akaona munthu aliyense wamphamvu kapena wolimba mtima, anali kum’tenga kuti akhale msilikali wake.+ 1 Samueli 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo onse ku Afeki, pamene Aisiraeli anamanga msasa pafupi ndi kasupe amene anali ku Yezereeli.+
52 M’masiku onse a Sauli, Afilisiti anali kupanikizidwa ndi nkhondo.+ Ndipo Sauli akaona munthu aliyense wamphamvu kapena wolimba mtima, anali kum’tenga kuti akhale msilikali wake.+
29 Ndiyeno Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo onse ku Afeki, pamene Aisiraeli anamanga msasa pafupi ndi kasupe amene anali ku Yezereeli.+