1 Samueli 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno masiku amenewo zinachitika kuti Afilisiti anayamba kusonkhanitsa asilikali awo kuti akamenyane ndi Isiraeli.+ Choncho, Akisi anauza Davide kuti: “Ndikukhulupirira kuti ukudziwa kuti iwe ndi anthu ako muyenera kupita ndi ine kunkhondo.”+
28 Ndiyeno masiku amenewo zinachitika kuti Afilisiti anayamba kusonkhanitsa asilikali awo kuti akamenyane ndi Isiraeli.+ Choncho, Akisi anauza Davide kuti: “Ndikukhulupirira kuti ukudziwa kuti iwe ndi anthu ako muyenera kupita ndi ine kunkhondo.”+