-
1 Samueli 29:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno akalonga a Afilisiti anayamba kunena kuti: “Kodi Aheberi+ awa akufuna chiyani kuno?” Pamenepo Akisi anayankha akalonga a Afilisitiwo kuti: “Kodi uyu si Davide, mtumiki wa Sauli, mfumu ya Isiraeli? Iyetu wakhala ndi ine kuno kwa chaka chimodzi kapena ziwiri,+ ndipo kuyambira tsiku limene anathawira kwa ine kufikira lero, sindinam’peze+ ndi chifukwa ngakhale chimodzi.”
-