1 Samueli 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo m’dziko lonse la Isiraeli munalibe wosula zitsulo. Izi zinali choncho chifukwa Afilisiti anati: “Aheberi asasule lupanga kapena mkondo.”+ 2 Akorinto 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi iwo ndi Aheberi? Inenso ndine Mheberi.+ Kodi ndi Aisiraeli? Inenso ndine Mwisiraeli. Kapena iwo ndi mbewu ya Abulahamu? Inenso chimodzimodzi.+
19 Ndipo m’dziko lonse la Isiraeli munalibe wosula zitsulo. Izi zinali choncho chifukwa Afilisiti anati: “Aheberi asasule lupanga kapena mkondo.”+
22 Kodi iwo ndi Aheberi? Inenso ndine Mheberi.+ Kodi ndi Aisiraeli? Inenso ndine Mwisiraeli. Kapena iwo ndi mbewu ya Abulahamu? Inenso chimodzimodzi.+