1 Samueli 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo onse ku Afeki, ndipo Aisiraeli anamanga msasa pafupi ndi kasupe wa ku Yezereeli.+
29 Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo onse ku Afeki, ndipo Aisiraeli anamanga msasa pafupi ndi kasupe wa ku Yezereeli.+