Yoswa 19:17, 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maere a 4+ anagwera Isakara,+ kapena kuti ana a Isakara motsatira mabanja awo. 18 Malire a gawo lawo anakafika ku Yezereeli,+ Kesulotu, Sunemu,+ 1 Samueli 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Davide anadzuka mʼmamawa pamodzi ndi amuna amene ankayenda naye nʼkubwerera kudziko la Afilisiti. Koma Afilisitiwo anapita ku Yezereeli.+
17 Maere a 4+ anagwera Isakara,+ kapena kuti ana a Isakara motsatira mabanja awo. 18 Malire a gawo lawo anakafika ku Yezereeli,+ Kesulotu, Sunemu,+
11 Choncho Davide anadzuka mʼmamawa pamodzi ndi amuna amene ankayenda naye nʼkubwerera kudziko la Afilisiti. Koma Afilisitiwo anapita ku Yezereeli.+