Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 3:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Zitatero, mfumu inayamba kuimba nyimbo yolira Abineri kuti:

      “Kodi zoona Abineri afe imfa ngati ya munthu wopanda pake?+

  • 2 Mbiri 35:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Yeremiya+ anayamba kuimbira Yosiya nyimbo ya maliro.+ Oimba onse aamuna ndi aakazi+ amanenabe za Yosiya m’nyimbo zawo zoimba polira mpaka lero. Nyimbo zimenezi zinakhazikitsidwa ngati lamulo mu Isiraeli, ndipo zinalembedwa m’nyimbo zoimba polira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena