Yeremiya 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Chitani zinthu mozindikira anthu inu, ndipo itanani akazi oimba nyimbo zoimba polira kuti abwere.+ Tumizani anthu kuti akaitane akazi odziwa kulira maliro,+ Yeremiya 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma tamverani mawu a Yehova akazi inu, ndipo mutchere khutu ku mawu otuluka m’kamwa mwake. Kenako muphunzitse ana anu aakazi kulira maliro+ ndipo mkazi aliyense aphunzitse mnzake nyimbo yoimba polira.+
17 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Chitani zinthu mozindikira anthu inu, ndipo itanani akazi oimba nyimbo zoimba polira kuti abwere.+ Tumizani anthu kuti akaitane akazi odziwa kulira maliro,+
20 Koma tamverani mawu a Yehova akazi inu, ndipo mutchere khutu ku mawu otuluka m’kamwa mwake. Kenako muphunzitse ana anu aakazi kulira maliro+ ndipo mkazi aliyense aphunzitse mnzake nyimbo yoimba polira.+