Yobu 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yobu atamva zimenezi anaimirira n’kung’amba+ malaya ake akunja odula manja. Anametanso tsitsi+ kumutu kwake, kenako anagwada pansi+ n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ Yeremiya 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Anthu onse a m’dzikoli, osasiyapo aliyense, adzafa ndithu. Sadzaikidwa m’manda+ ndipo anthu sadzadziguguda pachifuwa chifukwa cha iwo. Palibe aliyense amene adzadzichekacheka+ kapena kumeta mpala chifukwa cha iwo.+ Mika 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Meta mpala ndi kuchotsa tsitsi lonse chifukwa cha ana ako aamuna amene unali kuwakonda.+ Meta mpala mpaka ufanane ndi wa chiwombankhanga, chifukwa chakuti ana akowo akusiya ndipo apita kudziko lina.”+
20 Yobu atamva zimenezi anaimirira n’kung’amba+ malaya ake akunja odula manja. Anametanso tsitsi+ kumutu kwake, kenako anagwada pansi+ n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+
6 ‘Anthu onse a m’dzikoli, osasiyapo aliyense, adzafa ndithu. Sadzaikidwa m’manda+ ndipo anthu sadzadziguguda pachifuwa chifukwa cha iwo. Palibe aliyense amene adzadzichekacheka+ kapena kumeta mpala chifukwa cha iwo.+
16 Meta mpala ndi kuchotsa tsitsi lonse chifukwa cha ana ako aamuna amene unali kuwakonda.+ Meta mpala mpaka ufanane ndi wa chiwombankhanga, chifukwa chakuti ana akowo akusiya ndipo apita kudziko lina.”+