5 kunabwera amuna ochokera ku Sekemu,+ ku Silo+ ndi ku Samariya.+ Iwo analipo 80 ndipo anabwera atameta ndevu,+ atadzichekacheka ndiponso atang’amba zovala zawo.+ Amunawa anabwera ndi nsembe yambewu ndi lubani+ m’manja mwawo kuti adzazipereke kunyumba ya Yehova.