Yeremiya 41:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kunabwera amuna 80 ochokera ku Sekemu,+ ku Silo+ ndi ku Samariya.+ Iwo anabwera atameta ndevu, atangʼamba zovala zawo ndiponso atadzichekacheka.+ Amunawa anabwera atanyamula nsembe yambewu komanso lubani+ kuti adzazipereke kunyumba ya Yehova.
5 kunabwera amuna 80 ochokera ku Sekemu,+ ku Silo+ ndi ku Samariya.+ Iwo anabwera atameta ndevu, atangʼamba zovala zawo ndiponso atadzichekacheka.+ Amunawa anabwera atanyamula nsembe yambewu komanso lubani+ kuti adzazipereke kunyumba ya Yehova.