Deuteronomo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu.+ Musamadzichekecheke+ kapena kumeta+ nsidze* zanu chifukwa cha anthu akufa. Yeremiya 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Anthu onse a m’dzikoli, osasiyapo aliyense, adzafa ndithu. Sadzaikidwa m’manda+ ndipo anthu sadzadziguguda pachifuwa chifukwa cha iwo. Palibe aliyense amene adzadzichekacheka+ kapena kumeta mpala chifukwa cha iwo.+
14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu.+ Musamadzichekecheke+ kapena kumeta+ nsidze* zanu chifukwa cha anthu akufa.
6 ‘Anthu onse a m’dzikoli, osasiyapo aliyense, adzafa ndithu. Sadzaikidwa m’manda+ ndipo anthu sadzadziguguda pachifuwa chifukwa cha iwo. Palibe aliyense amene adzadzichekacheka+ kapena kumeta mpala chifukwa cha iwo.+