Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 63:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Inutu ndinu Atate wathu.+ Ngakhale kuti Abulahamu sanatidziwe ndipo Isiraeli sanatizindikire, inuyo Yehova ndinu Atate wathu. Dzina lanu ndinu Wotiwombola wakalekale.+

  • Yesaya 64:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komatu inu Yehova, inu ndinu Atate wathu.+ Ife ndife dongo+ ndipo inu ndinu Wotiumba.+ Tonsefe ndife ntchito ya manja anu.+

  • Yeremiya 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ine ndanena kuti, ‘Mokondwera ndinakuikani pakati pa ana anga ndi kukupatsani dziko labwino,+ cholowa chimene mitundu yambiri ya anthu imachisirira!’ Ndipo ndinanenanso kuti, ‘Anthu inu mudzandiitana kuti, “Atate wanga!”+ ndipo mudzandilondola osabwerera.’

  • 1 Akorinto 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 kwa ife Mulungu alipo mmodzi yekha basi+ amene ndi Atate.+ Iye ndi amene zinthu zonse zinachokera mwa iye, ndipo ifeyo ndife ake.+ Ndipo pali Ambuye+ mmodzi, Yesu Khristu,+ amene zinthu zonse zinakhalapo kudzera mwa iye,+ ndipo ifeyo kudzera mwa iyeyo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena