Levitiko 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Asamete mpala mitu yawo,+ asamete ndevu za m’masaya mwawo+ ndipo asadzitemeteme thupi lawo.+