Levitiko 19:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Musamete ndevu zanu zotsikira m’masaya ndipo musadule nsonga za ndevu zanu.*+ Yeremiya 48:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Mutu uliwonse wametedwa mpala,+ ndipo ndevu zonse n’zometa.+ M’manja monse ndi mochekekachekeka,+ ndipo anthu onse amanga ziguduli m’chiuno mwawo.’”+
37 Mutu uliwonse wametedwa mpala,+ ndipo ndevu zonse n’zometa.+ M’manja monse ndi mochekekachekeka,+ ndipo anthu onse amanga ziguduli m’chiuno mwawo.’”+