28 Iwo anayamba kuitana mokuwa kwambiri n’kumadzicheka+ ndi mipeni ndi mikondo ing’onoing’ono malinga ndi mwambo wawo, mpaka magazi anayamba kutuluka ndi kuyenderera pamatupi awo.
5 Gaza+ adzameta mpala+ chifukwa cha chisoni. Asikeloni+ amuwononga ndi kumukhalitsa chete. Inu otsala a m’chigwa cha Gaza ndi Asikeloni, mudzadzichekacheka kufikira liti?+