Levitiko 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “‘Musamadzicheke chifukwa cha munthu wakufa,+ ndipo musamadziteme zizindikiro. Ine ndine Yehova. Deuteronomo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu.+ Musamadzichekecheke+ kapena kumeta+ nsidze* zanu chifukwa cha anthu akufa.
14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu.+ Musamadzichekecheke+ kapena kumeta+ nsidze* zanu chifukwa cha anthu akufa.