Yeremiya 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 khamu lonse la anthu a mitundu yosiyanasiyana, mafumu onse a dziko la Uzi,+ mafumu onse a dziko la Afilisiti,+ Asikeloni,+ Gaza,+ Ekironi+ ndi otsala onse a ku Asidodi,+ Zekariya 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Asikeloni adzaona zimenezi ndipo adzachita mantha. Gaza adzamva ululu waukulu. Izi zidzachitikiranso Ekironi+ chifukwa chakuti amene anali kumudalira+ adzachita manyazi. Ku Gaza sikudzakhalanso mfumu ndipo m’dziko la Asikeloni simudzakhalanso anthu.+
20 khamu lonse la anthu a mitundu yosiyanasiyana, mafumu onse a dziko la Uzi,+ mafumu onse a dziko la Afilisiti,+ Asikeloni,+ Gaza,+ Ekironi+ ndi otsala onse a ku Asidodi,+
5 Asikeloni adzaona zimenezi ndipo adzachita mantha. Gaza adzamva ululu waukulu. Izi zidzachitikiranso Ekironi+ chifukwa chakuti amene anali kumudalira+ adzachita manyazi. Ku Gaza sikudzakhalanso mfumu ndipo m’dziko la Asikeloni simudzakhalanso anthu.+