Yeremiya 47:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Gaza adzameta mpala chifukwa cha chisoni. Asikeloni amukhalitsa chete.+ Inu otsala amʼchigwa cha Gaza ndi Asikeloni,Kodi mupitiriza kudzichekacheka mpaka liti?+
5 Gaza adzameta mpala chifukwa cha chisoni. Asikeloni amukhalitsa chete.+ Inu otsala amʼchigwa cha Gaza ndi Asikeloni,Kodi mupitiriza kudzichekacheka mpaka liti?+