Yeremiya 47:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Gaza+ adzameta mpala+ chifukwa cha chisoni. Asikeloni+ amuwononga ndi kumukhalitsa chete. Inu otsala a m’chigwa cha Gaza ndi Asikeloni, mudzadzichekacheka kufikira liti?+
5 Gaza+ adzameta mpala+ chifukwa cha chisoni. Asikeloni+ amuwononga ndi kumukhalitsa chete. Inu otsala a m’chigwa cha Gaza ndi Asikeloni, mudzadzichekacheka kufikira liti?+