Yeremiya 48:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Mutu uliwonse wametedwa mpala,+Ndipo ndevu zonse nʼzometa. Mʼmanja monse ndi mochekekachekeka,+Ndipo anthu onse amanga ziguduli mʼchiuno mwawo.+
37 Mutu uliwonse wametedwa mpala,+Ndipo ndevu zonse nʼzometa. Mʼmanja monse ndi mochekekachekeka,+Ndipo anthu onse amanga ziguduli mʼchiuno mwawo.+