-
Genesis 37:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Atatero Yakobo anangʼamba zovala zake nʼkuvala chiguduli mʼchiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.
-