Genesis 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+ Ezekieli 27:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Adzadzimeta mpala chifukwa cha iwe+ ndi kuvala ziguduli+ ndipo adzakulirira mowawidwa mtima.+ Danieli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+
34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+
3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+