Yesaya 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 N’chifukwa chake ndanena kuti: “Musandiyang’anitsitse. Ine ndikulira mopwetekedwa mtima+ ndipo anthu inu musaumirire kunditonthoza pamene ndikulirira mwana wamkazi wa anthu anga, yemwe walandidwa katundu.+
4 N’chifukwa chake ndanena kuti: “Musandiyang’anitsitse. Ine ndikulira mopwetekedwa mtima+ ndipo anthu inu musaumirire kunditonthoza pamene ndikulirira mwana wamkazi wa anthu anga, yemwe walandidwa katundu.+