Levitiko 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “‘Musamadzicheke chifukwa cha munthu wakufa,+ ndipo musamadziteme zizindikiro. Ine ndine Yehova. 1 Mafumu 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo anayamba kuitana mokuwa kwambiri n’kumadzicheka+ ndi mipeni ndi mikondo ing’onoing’ono malinga ndi mwambo wawo, mpaka magazi anayamba kutuluka ndi kuyenderera pamatupi awo. Yeremiya 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Anthu onse a m’dzikoli, osasiyapo aliyense, adzafa ndithu. Sadzaikidwa m’manda+ ndipo anthu sadzadziguguda pachifuwa chifukwa cha iwo. Palibe aliyense amene adzadzichekacheka+ kapena kumeta mpala chifukwa cha iwo.+
28 Iwo anayamba kuitana mokuwa kwambiri n’kumadzicheka+ ndi mipeni ndi mikondo ing’onoing’ono malinga ndi mwambo wawo, mpaka magazi anayamba kutuluka ndi kuyenderera pamatupi awo.
6 ‘Anthu onse a m’dzikoli, osasiyapo aliyense, adzafa ndithu. Sadzaikidwa m’manda+ ndipo anthu sadzadziguguda pachifuwa chifukwa cha iwo. Palibe aliyense amene adzadzichekacheka+ kapena kumeta mpala chifukwa cha iwo.+