Genesis 24:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo mwamunayo anagwada pansi n’kuwerama pamaso pa Yehova+ Ekisodo 34:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nthawi yomweyo, Mose anagwada n’kuweramira pansi.+ Nehemiya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo anaimirira pomwepo+ ndipo anawerenga mokweza buku la chilamulo+ cha Yehova Mulungu wawo kwa maola atatu.*+ Kwa maola enanso atatu anali kuulula machimo awo+ ndi kugwadira Yehova Mulungu wawo.+
3 Iwo anaimirira pomwepo+ ndipo anawerenga mokweza buku la chilamulo+ cha Yehova Mulungu wawo kwa maola atatu.*+ Kwa maola enanso atatu anali kuulula machimo awo+ ndi kugwadira Yehova Mulungu wawo.+