-
Nehemiya 8:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ezara anawerenga+ mokweza bukulo m’bwalo lalikulu limene linali pafupi ndi Chipata cha Kumadzi, kuyambira m’mawa+ mpaka masana. Anali kuwerenga bukuli pamaso pa amuna, akazi ndi ana amene akanatha kumvetsera ndi kuzindikira. Anthu onse anatchera khutu kuti amve+ zimene zinali m’buku la chilamuloli.
-