Luka 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako anabwera ku Nazareti,+ kumene analeredwa. Malinga ndi chizolowezi chake pa tsiku la sabata, analowa m’sunagoge,+ ndi kuimirira kuti awerenge Malemba. Machitidwe 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chilamulo ndi Zolemba za aneneri zitawerengedwa pamaso pa anthu,+ atsogoleri+ a sunagoge anawatumizira mawu akuti: “Amuna inu, abale athu, ngati muli ndi mawu alionse olimbikitsa nawo anthu, lankhulani.” Machitidwe 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera m’mabuku a Mose, chifukwa mabuku amenewa amawerengedwa mokweza m’masunagoge sabata lililonse.”+
16 Kenako anabwera ku Nazareti,+ kumene analeredwa. Malinga ndi chizolowezi chake pa tsiku la sabata, analowa m’sunagoge,+ ndi kuimirira kuti awerenge Malemba.
15 Chilamulo ndi Zolemba za aneneri zitawerengedwa pamaso pa anthu,+ atsogoleri+ a sunagoge anawatumizira mawu akuti: “Amuna inu, abale athu, ngati muli ndi mawu alionse olimbikitsa nawo anthu, lankhulani.”
21 Pakuti kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera m’mabuku a Mose, chifukwa mabuku amenewa amawerengedwa mokweza m’masunagoge sabata lililonse.”+