Machitidwe 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera mʼmabuku a Mose, popeza mabuku amenewa amawerengedwa mokweza mʼmasunagoge sabata lililonse.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:21 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 109, 111 Nsanja ya Olonda,5/1/1995, tsa. 116/15/1990, tsa. 13
21 Chifukwa kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera mʼmabuku a Mose, popeza mabuku amenewa amawerengedwa mokweza mʼmasunagoge sabata lililonse.”+
15:21 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 109, 111 Nsanja ya Olonda,5/1/1995, tsa. 116/15/1990, tsa. 13