Machitidwe 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera m’mabuku a Mose, chifukwa mabuku amenewa amawerengedwa mokweza m’masunagoge sabata lililonse.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:21 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 109, 111 Nsanja ya Olonda,5/1/1995, tsa. 116/15/1990, tsa. 13
21 Pakuti kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera m’mabuku a Mose, chifukwa mabuku amenewa amawerengedwa mokweza m’masunagoge sabata lililonse.”+
15:21 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 109, 111 Nsanja ya Olonda,5/1/1995, tsa. 116/15/1990, tsa. 13