Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Mose anaitana Aisiraeli+ onse n’kuwauza kuti: “Inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo+ zimene ndikukuuzani lero, ndipo muziphunzire ndi kuzitsatira mosamala.+

  • Luka 8:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Pakuti amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+

  • Machitidwe 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pamenepo panali mayi wina dzina lake Lidiya ndipo anali wolambira Mulungu. Iyeyu anali wochokera kumzinda wa Tiyatira+ ndipo anali wogulitsa nsalu ndi zovala zofiirira. Pamene anali kumvetsera, Yehova anatsegula kwambiri mtima wake+ kuti atchere khutu ku zimene Paulo anali kunena.

  • Machitidwe 17:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma anthu a ku Bereya anali a mtima wofuna kuphunzira kuposa a ku Tesalonika aja. Iwowa analandira mawu a Mulungu ndi chidwi chachikulu kwambiri, ndipo tsiku ndi tsiku anali kufufuza+ Malemba+ mosamala kuti atsimikizire ngati zimene anamvazo zinalidi zoona.+

  • Aheberi 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiye chifukwa chake n’kofunika kuti tiganizire mozama, kuposa nthawi zonse, zinthu zimene tinamva,+ kuti tisatengeke pang’onopang’ono n’kusiya chikhulupiriro.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena