Mateyu 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti amene ali nazo, adzawonjezeredwa zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka.+ Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+ Mateyu 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pakuti amene ali nazo, adzawonjezeredwa zambiri ndipo adzakhala nazo zambiri, koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+ Maliko 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti amene ali nazo adzapatsidwa zochuluka. Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.”+ Luka 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ‘Ndithu ndikukuuzani, Aliyense amene ali nazo, adzamuwonjezera zochuluka, koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+
12 Pakuti amene ali nazo, adzawonjezeredwa zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka.+ Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+
29 Pakuti amene ali nazo, adzawonjezeredwa zambiri ndipo adzakhala nazo zambiri, koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+
25 Pakuti amene ali nazo adzapatsidwa zochuluka. Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.”+
26 ‘Ndithu ndikukuuzani, Aliyense amene ali nazo, adzamuwonjezera zochuluka, koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+