Mateyu 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa amene ali nazo, adzapatsidwa zinanso zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka. Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhale zimene akuganiza kuti ali nazo.+
12 Chifukwa amene ali nazo, adzapatsidwa zinanso zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka. Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhale zimene akuganiza kuti ali nazo.+