Mateyu 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti amene ali nazo, adzawonjezeredwa zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka.+ Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+ Mateyu 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mbuye wake anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe! Unakhulupirika pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti uziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’ Luka 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Pakuti amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+ Luka 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ‘Ndithu ndikukuuzani, Aliyense amene ali nazo, adzamuwonjezera zochuluka, koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+
12 Pakuti amene ali nazo, adzawonjezeredwa zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka.+ Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+
23 Mbuye wake anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe! Unakhulupirika pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti uziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’
18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Pakuti amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+
26 ‘Ndithu ndikukuuzani, Aliyense amene ali nazo, adzamuwonjezera zochuluka, koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+