-
Mateyu 25:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mbuye wake anamuyankha kuti: ‘Wachita bwino kwambiri, ndiwe kapolo wabwino komanso wokhulupirika! Unakhulupirika pa zinthu zochepa, ndikuika kuti uziyangʼanira zinthu zambiri. Sangalala limodzi ndi ine mbuye wako.’
-