Mateyu 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mbuye wake anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe! Unakhulupirika pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti uziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:23 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2021, tsa. 22 Nsanja ya Olonda,3/1/2004, tsa. 176/15/1995, tsa. 175/1/1990, tsa. 9
23 Mbuye wake anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe! Unakhulupirika pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti uziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’
25:23 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2021, tsa. 22 Nsanja ya Olonda,3/1/2004, tsa. 176/15/1995, tsa. 175/1/1990, tsa. 9