Maliko 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti amene ali nazo adzapatsidwa zochuluka. Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.”+ Luka 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Pakuti amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+
25 Pakuti amene ali nazo adzapatsidwa zochuluka. Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.”+
18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Pakuti amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+