Mateyu 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti amene ali nazo, adzawonjezeredwa zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka.+ Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+ Maliko 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti amene ali nazo adzapatsidwa zochuluka. Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.”+ Luka 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Pakuti amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+ Yohane 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nthambi iliyonse mwa ine yosabala zipatso amaidula,+ ndipo iliyonse yobala zipatso amaiyeretsa mwa kuitengulira+ kuti ibale zipatso zambiri.+
12 Pakuti amene ali nazo, adzawonjezeredwa zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka.+ Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+
25 Pakuti amene ali nazo adzapatsidwa zochuluka. Koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.”+
18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Pakuti amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+
2 Nthambi iliyonse mwa ine yosabala zipatso amaidula,+ ndipo iliyonse yobala zipatso amaiyeretsa mwa kuitengulira+ kuti ibale zipatso zambiri.+