Mateyu 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma iye anayankha kuti: “Mbewu iliyonse imene sinabzalidwe ndi Atate wanga wakumwamba idzazulidwa.+ Aheberi 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ikatulutsa minga ndi mitula, imakanidwa ndipo imatsala pang’ono kutembereredwa.+ Mapeto ake imatenthedwa.+
13 Koma iye anayankha kuti: “Mbewu iliyonse imene sinabzalidwe ndi Atate wanga wakumwamba idzazulidwa.+
8 Koma ikatulutsa minga ndi mitula, imakanidwa ndipo imatsala pang’ono kutembereredwa.+ Mapeto ake imatenthedwa.+