Yohane 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati munthu sakhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja monga nthambi ndipo amauma. Nthambi zoterozo anthu amazisonkhanitsa ndi kuziponya pamoto ndipo zimapsa.+ Machitidwe 5:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Choncho mmene zinthu zilili panopa, ndikukuuzani kuti, Alekeni amuna amenewa musalimbane nawo. Chifukwa ngati zolinga zawo kapena ntchito iyi ikuchokera kwa anthu, sipita patali.+
6 Ngati munthu sakhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja monga nthambi ndipo amauma. Nthambi zoterozo anthu amazisonkhanitsa ndi kuziponya pamoto ndipo zimapsa.+
38 Choncho mmene zinthu zilili panopa, ndikukuuzani kuti, Alekeni amuna amenewa musalimbane nawo. Chifukwa ngati zolinga zawo kapena ntchito iyi ikuchokera kwa anthu, sipita patali.+