2 Petulo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngati zinthu zimenezi zili mwa inu ndipo zikusefukira, zidzakutetezani kuti musakhale ozilala kapena osabala zipatso+ pa zimene mukuchita mogwirizana ndi kumudziwa molondola Ambuye wathu Yesu Khristu.
8 Ngati zinthu zimenezi zili mwa inu ndipo zikusefukira, zidzakutetezani kuti musakhale ozilala kapena osabala zipatso+ pa zimene mukuchita mogwirizana ndi kumudziwa molondola Ambuye wathu Yesu Khristu.