1 Mbiri 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Davide anauza mpingo wonse kuti:+ “Tsopano tamandani+ Yehova Mulungu wanu!” Choncho mpingo wonse unayamba kutamanda Yehova Mulungu wa makolo awo, ndipo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ kwa Yehova ndi kwa mfumu. Nehemiya 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Ezara anatamanda Yehova+ Mulungu woona, Mulungu wamkulu. Atatero anthu onse anakweza manja awo m’mwamba+ ndi kuyankha kuti, “Ame! Ame!”*+ Ndiyeno anthuwo anagwada+ ndi kuwerama pamaso pa Yehova mpaka nkhope zawo pansi.+ Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani timuweramire ndi kumupembedza.+Tiyeni tigwade+ pamaso pa Yehova amene ndiye Wotipanga.+
20 Kenako Davide anauza mpingo wonse kuti:+ “Tsopano tamandani+ Yehova Mulungu wanu!” Choncho mpingo wonse unayamba kutamanda Yehova Mulungu wa makolo awo, ndipo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ kwa Yehova ndi kwa mfumu.
6 Kenako Ezara anatamanda Yehova+ Mulungu woona, Mulungu wamkulu. Atatero anthu onse anakweza manja awo m’mwamba+ ndi kuyankha kuti, “Ame! Ame!”*+ Ndiyeno anthuwo anagwada+ ndi kuwerama pamaso pa Yehova mpaka nkhope zawo pansi.+