1 Mbiri 16:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli kuyambira kalekale mpaka kalekale.’”+Ndiyeno anthu onse ananena kuti, “Ame!”* n’kutamanda Yehova.+ Salimo 134:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene mukupemphera mutakweza manja anu, muzikhala oyera,+Ndipo tamandani Yehova.+ Salimo 145:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 145 Ndidzakukwezani, inu Mfumu ndi Mulungu wanga,+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Aefeso 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamandike Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti watidalitsa+ ndi dalitso lililonse lauzimu m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu.
36 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli kuyambira kalekale mpaka kalekale.’”+Ndiyeno anthu onse ananena kuti, “Ame!”* n’kutamanda Yehova.+
145 Ndidzakukwezani, inu Mfumu ndi Mulungu wanga,+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
3 Atamandike Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti watidalitsa+ ndi dalitso lililonse lauzimu m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu.