Genesis 24:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo mwamunayo anagwada pansi n’kuwerama pamaso pa Yehova+ Ekisodo 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova wacheukira+ ana a Isiraeli, ndi kutinso waona nsautso yawo,+ anagwada ndi kuweramira pansi.+
31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova wacheukira+ ana a Isiraeli, ndi kutinso waona nsautso yawo,+ anagwada ndi kuweramira pansi.+