Genesis 50:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano Yosefe analumbiritsa ana a Isiraeliwo, kuti: “Ndithu Mulungu adzakucheukirani. Akadzatero mudzanyamule mafupa anga pochoka kuno.”+ Ekisodo 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho Mose anatenga mafupa a Yosefe chifukwa Yosefe analumbiritsa ana a Isiraeli, kuti: “Ndithudi, Mulungu adzakukumbukirani,+ ndipo pochoka kuno mudzatenge mafupa anga.”+
25 Tsopano Yosefe analumbiritsa ana a Isiraeliwo, kuti: “Ndithu Mulungu adzakucheukirani. Akadzatero mudzanyamule mafupa anga pochoka kuno.”+
19 Choncho Mose anatenga mafupa a Yosefe chifukwa Yosefe analumbiritsa ana a Isiraeli, kuti: “Ndithudi, Mulungu adzakukumbukirani,+ ndipo pochoka kuno mudzatenge mafupa anga.”+