Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 43:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Iwo anayankha kuti: “Kapolo wanu bambo athu ali bwino. Adakali ndi moyo.” Atatero anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+

  • 2 Mbiri 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ana onse a Isiraeli anali kuonerera pamene moto unali kutsika, ndiponso pamene ulemerero wa Yehova unaonekera pamwamba pa nyumbayo. Ataona zimenezi, nthawi yomweyo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ ndi kuyamika Yehova, “chifukwa iye ndi wabwino,+ pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhala mpaka kalekale.”+

  • Nehemiya 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako Ezara anatamanda Yehova+ Mulungu woona, Mulungu wamkulu. Atatero anthu onse anakweza manja awo m’mwamba+ ndi kuyankha kuti, “Ame! Ame!”*+ Ndiyeno anthuwo anagwada+ ndi kuwerama pamaso pa Yehova mpaka nkhope zawo pansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena