Salimo 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ubwino wanu,+ umene mwasungira anthu okuopani ndi wochuluka kwambiri!+Ubwino umenewu mwapereka kwa anthu othawira kwa inu.Mwaupereka kwa iwo, ana a anthu akuona.+ Mateyu 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anamuyankha kuti: “N’chifukwa chiyani ukundifunsa chimene chili chabwino? Pali Mmodzi yekha amene ali wabwino.+ Chotero ngati ukufuna kukapeza moyo, uzisunga malamulo nthawi zonse.”+
19 Ubwino wanu,+ umene mwasungira anthu okuopani ndi wochuluka kwambiri!+Ubwino umenewu mwapereka kwa anthu othawira kwa inu.Mwaupereka kwa iwo, ana a anthu akuona.+
17 Iye anamuyankha kuti: “N’chifukwa chiyani ukundifunsa chimene chili chabwino? Pali Mmodzi yekha amene ali wabwino.+ Chotero ngati ukufuna kukapeza moyo, uzisunga malamulo nthawi zonse.”+