Rute 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Naomi anauza mpongozi wakeyo kuti: “Yehova amene sanaleke kusonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa amoyo ndi akufa,+ am’dalitse munthu ameneyu.”+ Ndipo Naomi anapitiriza kuti: “Munthuyutu ndi wachibale wathu.+ Ndi mmodzi wa otiwombola.”+ Yeremiya 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anabwera kwa ine kuchokera kutali, ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale.+ N’chifukwa chake ndakukoka mwa kukoma mtima kwanga kosatha.+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+
20 Pamenepo Naomi anauza mpongozi wakeyo kuti: “Yehova amene sanaleke kusonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa amoyo ndi akufa,+ am’dalitse munthu ameneyu.”+ Ndipo Naomi anapitiriza kuti: “Munthuyutu ndi wachibale wathu.+ Ndi mmodzi wa otiwombola.”+
3 Yehova anabwera kwa ine kuchokera kutali, ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale.+ N’chifukwa chake ndakukoka mwa kukoma mtima kwanga kosatha.+
22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+