Rute 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Boazi anafika kuchokera ku Betelehemu ndipo anauza okololawo kuti: “Yehova akhale nanu.”+ Iwo anayankha mwa nthawi zonse kuti: “Yehova akudalitseni.”+ Rute 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atatero, Boazi anati: “Yehova akudalitse,+ mwana wanga. Kukoma mtima kosatha+ kumene wasonyeza panopa kukuposa koyamba kuja,+ popeza sunafune anyamata, kaya osauka kapena olemera. 2 Samueli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Davide anatumiza mithenga kwa amuna a ku Yabesi-giliyadi+ kuti akawauze kuti: “Yehova akudalitseni,+ chifukwa munasonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa mbuye wanu Sauli mwa kumuika m’manda.+
4 Kenako Boazi anafika kuchokera ku Betelehemu ndipo anauza okololawo kuti: “Yehova akhale nanu.”+ Iwo anayankha mwa nthawi zonse kuti: “Yehova akudalitseni.”+
10 Atatero, Boazi anati: “Yehova akudalitse,+ mwana wanga. Kukoma mtima kosatha+ kumene wasonyeza panopa kukuposa koyamba kuja,+ popeza sunafune anyamata, kaya osauka kapena olemera.
5 Choncho Davide anatumiza mithenga kwa amuna a ku Yabesi-giliyadi+ kuti akawauze kuti: “Yehova akudalitseni,+ chifukwa munasonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa mbuye wanu Sauli mwa kumuika m’manda.+