6 Zili choncho, Sauli anauza Akeni+ kuti: “Nyamukani,+ muchoke pakati pa Aamaleki kuti ndisakuwonongeni pamodzi nawo. Inuyo munasonyeza kukoma mtima kosatha kwa ana onse a Isiraeli+ atatuluka mu Iguputo.”+ Choncho Akeni anachokadi pakati pa Aamaleki.